
Chamba chathu simungafile nacho ayile – yachenjeza LUANAR
Advertisement Sukulu yaukachenjede ya Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources (LUANAR) yachenjeza aphunzitsi komaso ophunzira ake kuti asati maso bilubilu pa chamba chomwe sukuluyi ikulima ponena kuti nchopanda ukali. Malingana ndi uthenga …